Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kudzikuza

Kudzikuza

Miy 11:2; 13:10

Onaninso Miy 21:24

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 2Sa 6:6, 7​—Uza anachita zinthu modzikuza pogwira Likasa la Mulungu womwe sunali udindo wake; choncho Mulungu anamupha pomwepo chifukwa chochita zinthu mopanda ulemu

    • 2Mb 26:16-21​—Mfumu Uziya analangidwa chifukwa cha mtima wake wodzikuza