Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kunyada

Kunyada

Kunyada; kudzikweza

Sl 138:6; Miy 16:5, 18; Yak 4:6, 16

Onaninso Miy 21:4

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Est 5:9-14; 7:9, 10​—Hamani yemwe anali wodzitama sanasangalale Moredekai atakana kumugwadira ndipo pamapeto pake anaphedwa chifukwa cha kunyada

    • Eze 28:11-15, 17, 19​—Mfumu ya ku Turo inayamba kunyada chifukwa cha chuma komanso mphamvu zake kenako inaphedwa