Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kuganiza Bwino

Kuganiza Bwino

N’chifukwa chiyani Akhristu ayenera kumaganiza bwino?

Afi 4:5; Tit 3:2; Yak 3:17

Onaninso 1Ti 3:2, 3

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 18:23-33​—Yehova anachita zinthu moleza mtima polola Abulahamu kufunsa mafunso okhudza kuwonongedwa kwa Sodomu ndi Gomora

    • Ge 19:16-22, 30​—Yehova anamuganizira Loti polola zimene anapempha kuti athawire ku Zowari m’malo mothawira kumapiri

    • Yesu anasonyeza kuganiza bwino pochita zimene mayi wa ku Foinike anapempha chifukwa chakuti anasonyeza kuti anali ndi chikhulupiriro chachikulu