Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zosangalatsa

Zosangalatsa

Kodi n’kulakwa kuti Akhristu azichita zosangalatsa?

Mla 2:24; 3:12, 13; 4:6

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Mko 6:31, 32​—Ngakhale kuti anali wotanganidwa, Yesu anawalimbikitsa ophunzira ake kuti apeze malo abwino kuti apume

Ndi mfundo ziti zomwe zingatithandize kuti tisamalole zosangalatsa kutisokoneza kuchita zinthu zauzimu?

N’chifukwa chiyani tiyenera kupewa zosangalatsa zimene zimalimbikitsa chiwerewere?

N’chifukwa chiyani tiyenera kupewa zosangalatsa zimene zimalimbikitsa anthu kupsa mtima kapena kukhala ndi mzimu wampikisano?

N’chifukwa chiyani tiyenera kupewa zosangalatsa zimene zimalimbikitsa chiwawa?

Kodi Akhristu ayenera kupewa nthabwala zotani?

N’chifukwa chiyani tiyenera kuganizira chikumbumtima cha ena tikamasankha zosangalatsa?