Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Kudziletsa

Kudziletsa

Kodi Yehova amasonyeza bwanji kudziletsa?

Kodi ndi mbali ziti pa moyo wathu zomwe timafunika kudziletsa?

Miy 16:32; 25:28; 1Ak 9:25, 27

Onaninso 2Ti 2:23-25; Tit 1:7, 8

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 2Sa 16:5-14​—Mfumu Davide anadziletsa pamene Simeyi anamulankhula mawu onyoza komanso kumuchitira zinthu mopanda ulemu

    • 1Pe 2:21-23​—Mtumwi Petulo anafotokoza kuti Yesu anasonyeza kuleza mtima kwambiri pamene anthu ankamuchitira zachipongwe komanso kumuzunza

N’chiyani chingatithandize kuti tipitirize kudziletsa?

Lu 11:9-13; Aga 5:22, 23; Aef 4:23, 24; Akl 4:2

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Lu 11:5-8​—Yesu anafotokoza kufunika kopitiriza kupempha kuti tithandizidwe