Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Nkhondo

Nkhondo

N’chifukwa chiyani tiyenera kuyembekezera kuti m’nthawi yathu ino kuchitika nkhondo zambiri?

Mt 24:3, 4, 7, 8

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Da 11:40​—Mneneri Danieli analosera kuti m’masiku otsiriza mafumu awiri amphamvu adzakankhana kapena kuti kupikisana pa nkhondo

    • Chv 6:1-4​—Mtumwi Yohane anaona hatchi yofiira ngati moto yomwe ikuimira nkhondo ndipo wokwerapo wake “analoledwa kuchotsa mtendere padziko lapansi”

Kodi Yehova adzachita chiyani ndi nkhondo zimene anthu akumenya padzikoli?

N’chifukwa chiyani Akhristu samenya nawo nkhondo?

Kodi Yehova ndi Yesu adzamenya nkhondo yotani?

Kodi Akhristu oona amamenya nkhondo yotani?

Kodi Akhristu mumpingo angapewe bwanji kulimbikitsa nkhondo, kukangana kapena kubwezera anthu amene awalakwira?