Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake


Kodi mwazikonda zimene mwaphunzila?

Kodi mwazikonda zimene mwaphunzila?

Kodi mungafune kuphunzila zambili za Baibo?

Izi n’zocepa cabe pa zimene mungaphuzile m’buku lakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!​—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita.

Buku ili pamodzi na maphunzilo ake ni aulele. Tidzakhala okondwa kuphunzila namwe pa nthawi na malo amene mungasankhe.

M’maphunzilo a Baibo amenewa, mudzaphunzila nkhani zambili, kuphatikizapo izi:

  • Colinga ca Moyo

  • Mmene tingapezele mtendele weniweni

  • Mmene mabanja angakhalile acimwemwe

  • Zimene Baibo imatilonjeza kutsogolo

Kuti mulipeze buku limeneli na kupitiliza maphunzilo a Baibo, pemphani wa Mboni za Yehova, kapena tumizani pempho lanu pa jw.org.