Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake


Kodi n’zotheka kukapeza moyo wamuyaya wacisangalalo?

Kodi n’zotheka kukapeza moyo wamuyaya wacisangalalo?

Kodi mungayankhe kuti . . .

  • inde?

  • iyai?

  • olo kapena?

ZIMENE BAIBO IMAKAMBA

“Olungama adzalandila dziko lapansi, ndipo adzakhala mmenemo kwamuyaya.” SALIMO 37:29.

UBWINO WOKHULUPILILA ZIMENEZI

Tsogolo lokondweletsa komanso la mtendele ku banja lanu na mabwenzi anu. YEREMIYA 29:11.

Kukondwela na moyo, osati kwa kanthawi koma kwamuyaya.SALIMO 22:26.

KODI TINGAKHULUPILILEDI ZIMENE BAIBO IMALONJEZA?

Inde! Kuti mupeze cifukwa cake, onani maumboni atatu amene ali m’kabuku kano. Mitu yake ni iyi: