Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Ziwerengero Zonse za 2023

Ziwerengero Zonse za 2023
  • Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova: 85

  • Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 239

  • Mipingo Yonse: 118,177

  • Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 20,461,767

  • Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 22,312

  • Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira a: 8,816,562

  • Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 8,625,042

  • Kuwonjezereka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2022: 1.3

  • Obatizidwa Onse b: 269,517

  • Avereji ya Apainiya c Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,570,906

  • Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 738,457

  • Maola Onse Amene Tinalalikira: 1,791,490,713

  • Avereji ya Maphunziro a Baibulo d Mwezi Uliwonse: 7,281,212

Chaka cha utumiki cha 2023 chinayambira pa 1 September 2022, ndipo chinatha pa 31 August 2023.

a Wofalitsa ndi munthu amene amalalikira mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengerochi, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

b Kuti mudziwe zimene mungachite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?

c Mpainiya ndi wa Mboni wobatizidwa komanso wachitsanzo chabwino amene amadzipereka kuti azilalikira uthenga wabwino kwa maola enaake mwezi uliwonse.

d Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Phunziro la Baibulo Lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?