Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Laciŵili

Tsiku Laciŵili

“Tsiku ndi tsiku muzilengeza uthenga wabwino wa cipulumutso cake”​—Salimo 96:2

M’maŵa

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 53 na Pemphelo

  • 8:40 ‘Niyenela Kulengeza Uthenga Wabwino wa Ufumu’ (Luka 4:43)

  • 8:50 SEŴELO LALIKULU LA M’BAIBO:

    Uthenga Wabwino Wolalikidwa na Yesu: Mbali 1

    Kuwala Kwenikweni kwa Dziko—Gawo Laciŵili (Mateyu 2:​1-23; Luka 2:​1-38, 41-52; Yohane 1:9)

  • 9:25 Nyimbo Na. 69 na Zilengezo

  • 9:35 YOSIYILANA: Maulosi Okhudza Mesiya Anakwanilitsika!

    • • Pambuyo pa Mthenga (Malaki 3:1; 4:5; Mateyu 11:​10-14)

    • • Anabadwa kwa Namwali (Yesaya 7:14; Mateyu 1:​18, 22, 23)

    • • Anabadwila ku Betelehemu (Mika 5:2; Luka 2:​4-7)

    • • Anatetezedwa Ali Mwana (Hoseya 11:1; Mateyu 2:​13-15)

    • • Anachedwa Mnazareti (Yesaya 11:​1, 2; Mateyu 2:23)

    • • Anafika pa Nthawi Yoikika (Danieli 9:25; Luka 3:​1, 2, 21, 22)

  • 10:40 UBATIZO: Pitilizani ‘Kugonjela Uthenga Wabwino’ (2 Akorinto 9:13; 1 Timoteyo 4:​12-16; Aheberi 13:17)

  • 11:10 Nyimbo Na. 24 na Kupumula

Masana

  • 12:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:45 Nyimbo Na. 83

  • 12:50 YOSIYILANA: Seŵenzetsani Uthenga Wabwino Pogonjetsa Uthenga Woipa

    • • Mijedo Yovulaza (Yesaya 52:7)

    • • Cikumbumtima Covutitsidwa (1 Yohane 1:​7, 9)

    • • Zinthu Zimene Zikucitika Masiku Ano (Matthew 24:14)

    • • Zolefula (Mateyu 11:​28-30)

  • 13:35 YOSIYILANA: “Ofunitsitsa Kulengeza Uthenga Wabwino”

    • • Sinali Nchito ya Atumwi Okha (Aroma 1:15; 1 Atesalonika 1:8)

    • • Ni Mbali ya Kulambila (Aroma 1:9)

    • • Khalani Okonzeka Pokhala na Zida Zoyenela (Aefeso 6:15)

  • 14:15 VIDIYO: Mmene ‘Uthenga Wabwino Ukubalila Zipatso na Kufalikila Padziko Lonse’ (Akolose 1:6)

  • 14:40 Nyimbo Na. 35 na Zilengezo

  • 14:50 YOSIYILANA: Pitilizani Kulalikila Uthenga Wabwino

    • • Kulikonse Kumene Mungakhale (2 Timoteyo 4:5)

    • • Kulikonse Kumene Mulungu Angakutsogoleleni (Machitidwe 16:​6-10)

  • 15:15 Kodi Mudzacita Ciyani “Cifukwa ca Uthenga Wabwino”? (1 Akorinto 9:23; Yesaya 6:8)

  • 15:50 Nyimbo Na. 21 na Pemphelo Lothela