Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2010

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2010

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2010

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

BAIBULO

Baibulo la Dziko Latsopano M’Chichewa 11/1

Kodi Limafotokoza Zonse Zokhudza Yesu? 4/1

Kodi Ndi Louziridwa ndi Mulungu? 3/1

Kugwirizanitsa Ezekieli 18:20 ndi Eksodo 20:5, 3/15

Kukhulupirira Mabuku a Uthenga Wabwino, 3/1

Limasintha Anthu, 2/1, 5/1, 8/1, 11/1

Mateyu Anati Mawu a M’buku la Zekariya Ananena Ndi Yeremiya, 12/1

Mfundo 7 Zothandiza Kupindula ndi Kuwerenga Baibulo, 7/1

Wosindikiza Mabuku Amene Anathandiza Kulifalitsa, 7/1

MBIRI YA MOYO WANGA

Khulupirira Yehova (E. Schmidt), 9/1

Kutumikira Pamene Ntchito Yolalikira Yapita Patsogolo (H. Harris), 9/15

Mavuto Atithandiza Kudalira Yehova (A. Dello Stritto), 4/15

Mphamvu ya Choonadi cha m’Baibulo (V. Fraese), 12/15

Mulungu ‘Amachita Zinthu Zazikulu’ (M. Raj), 12/1

Zabwino Zimene Anachita Zapita Naye Limodzi, 11/15

Zochita Zambiri M’gulu la Yehova (V. Zubko), 10/15

MBONI ZA YEHOVA

Buku Lothandiza Achinyamata (Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri), 2/15

Bulgaria, 9/15

Chikumbutso, 3/1

‘Chopereka kwa Yehova,’ 11/15

Grenada, 9/1

Haiti, 12/1

“Kamandithandiza Kuwafika Pamtima Anthu” (kabuku ka Mitundu Yonse), 10/15

“Khalanibe pa Ubwenzi ndi Yehova,” Misonkhano Yachigawo, 3/1

Kuchita Mapemphero ndi Zipembedzo Zina, 6/1

Kukhala Tcheru (Finland), 7/15

Machiritso, 10/1

Msonkhano Wapachaka, 6/15

Mukuitanidwa! (Beteli), 8/15

Mwambo Womaliza Maphunziro a Gileadi, 2/1, 8/1

Nyumba za Ufumu, 5/1

Papua New Guinea, 3/1

South Africa, 6/1

Ukalamba Sungatilepheretse Kutumikira (Spain), 12/15

Zilumba Zakumpoto kwa Australia, 5/1

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

Amuna ndi Akazi Amasiye, 5/1

Apongozi, 2/1

Chaka Choyamba cha Ukwati, 8/1

‘Khalani Angwiro, Monga Atate Wanu Wakumwamba,’ 11/15

Khalanibe ‘Oyera Mtima,’ 3/15

Khalanibe Paubwenzi ndi Mulungu Zinthu Zikasintha, 3/15

Kodi Muyenera Kusunga Nthawi? 8/15

Kodi Muzisunga Sabata? 2/1

Kodi Mwana Wanu Angayankhe Bwanji? 12/15

Kodi N’kusaonadi Mtima? 6/1

Kubatizidwanso, 2/15

Kuganizira Makolo Amene Sali Pabanja, 12/1

Kukhala M’nyumba Imodzi ndi Anthu Ena, 2/15

Kulimba Mtima Potsatira Zimene Mumakhulupirira (Yeremiya), 5/1

Kulimbana ndi Nkhawa Ndiponso Chisoni, 10/1

Kupemphera, 10/1

Kupereka Zifukwa Pofuna Kudzikhululukira? 10/15

Kupeza Anzanu Enieni, 7/1

Kuphunzitsa Ana Kuti Adzathe Kudziimira Paokha, 5/1

Kusamalira Wachibale Amene Akudwala, 5/15

Kuthandiza Mnzanu Amene Akudwala, 7/1

Mabodza a Satana Asakusokonezeni, 2/15

Mfundo Zothandiza Kukhutira ndi Zimene Muli Nazo, 11/1

“Mpaka Imfa Idzatilekanitse,” 3/1

Mukhale Otetezeka, 4/15

‘Muzidzipereka pa Kuphunzitsa,’ 7/15

Muzikambirana ndi Ana Anu Nkhani Zokhudza Kugonana, 11/1

Muzilemekeza Mulungu Tsiku ndi Tsiku, 1/15

Muzilemekeza Okalamba, 5/15

Muziphunzitsa Luntha la Kuzindikira, 5/15

Muzitonthonza Anthu Oferedwa, 11/1

“Mwana Ali ndi Ufulu Wokula Mwauzimu,” 2/15

Ngati Mwamuna Kapena Mkazi Wanu Ali Wosakhulupirika, 6/15

Oona Mtima Nthawi Zonse, 3/1

Pewani Kuyendera Maganizo a Anthu Ena, 8/15

Thandizani Ana Kukonda Kuwerenga ndi Kuphunzira, 7/15

Thandizani Ana Kulidziwa Gulu la Yehova, 10/15

Thandizani Ana Kulimbana ndi Mavuto, 1/15

“Usaope Ndidzakuthandiza,” 7/15

Wodzichepetsa Ndiponso Wolimba Mtima (Yona), 1/1

Wokhulupirika Panthawi Yovuta (Petulo), 1/1

Zimene Tikuphunzira pa Chifundo cha Mulungu (Yona), 3/1

NKHANI ZOPHUNZIRA

Abale, Feserani Mzimu Ndipo Yesetsani Kuti Muyenerere Udindo, 5/15

Achinyamata, Khalani ndi Mtima Wokonda Kwambiri Kutumikira Yehova, 4/15

Achinyamata, Kodi Moyo Wanu Mudzaugwiritsa Ntchito Bwanji? 11/15

Achinyamata, Muzitsogoleredwa ndi Mawu a Mulungu, 11/15

Achinyamata, Pewani Kutengera Zochita za Anzanu, 11/15

Akazi, N’chifukwa Chiyani Muyenera Kugonjera Amuna Anu Monga Mutu? 5/15

Akhristu Oona Amadziwika Chifukwa cha Kugwirizana, 9/15

Amuna, Kodi Mumagonjera Khristu Monga Mutu Wanu? 5/15

Gulu Limodzi, M’busa Mmodzi, 3/15

Gwiritsani Ntchito Mwaluso “Lupanga la Mzimu,” 2/15

Imbirani Yehova, 12/15

‘Ino Ndiyo Nthawi Yeniyeni Yovomerezeka,’ 12/15

Khalani Odzipereka pa Kulambira Koona, 12/15

Khalani Otetezeka M’gulu la Anthu a Mulungu, 6/15

Kodi Mukhala Patsogolo Posonyeza Ulemu kwa Akhristu Anzanu? 10/15

Kodi Mukutsatira Khristu ndi Mtima Wonse? 4/15

Kodi Mumathandiza Kuti Misonkhano Yachikhristu Ikhale Yolimbikitsa? 10/15

Kodi Ndani Angathandize Anthu Ovutika? 8/15

Kodi pa Tsiku la Yehova Padzachitika Zotani? 7/15

Kodi Yesu Amasonyeza Bwanji Chilungamo cha Mulungu? 8/15

Kubatizidwa M’dzina la Atate, ndi la Mwana ndi la Mzimu Woyera, 3/15

Kuchita Zinthu Zauzimu Kumatsitsimula, 6/15

Kulankhula Mwaulemu Kumathandiza Kuti Tizikhala Bwino ndi Ena, 6/15

‘Lankhulani Mawu a Mulungu Molimba Mtima,’ 2/15

“Lingalirani za Mtundu wa Munthu Amene Muyenera Kukhala,” 7/15

Mgwirizano wa Akhristu Umalemekeza Mulungu, 9/15

Mmene Dipo Limatipulumutsira, 8/15

“Mtsogoleri Wanu Ndi Mmodzi, Khristu,” 9/15

Mtsogoleri Wathu Akuchita Zambiri Masiku Ano, 9/15

Musamaone Zinthu Zachabe, 4/15

Musamvetse Chisoni Mzimu Woyera wa Yehova, 5/15

Muzifunafuna Madalitso a Yehova ndi Mtima Wonse, 9/15

Muzigwira Nawo Mokwanira Ntchito Yokolola Mwauzimu, 7/15

Muzilimbikitsana Mumpingo, 6/15

Muzitsatira Lamulo la Kukoma Mtima Polankhula, 8/15

Muziyenda mwa Mzimu Kuti Mukwaniritse Kudzipereka Kwanu, 3/15

“Mzimu ndi Mkwatibwi Akunenabe Kuti: ‘Bwera’,” 2/15

“Mzimu Umafufuza . . . Zinthu Zozama za Mulungu,” 7/15

N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudzipereka kwa Yehova? 1/15

“Ndani Akudziwa Maganizo a Yehova?” 10/15

Ndife Anthu a Yehova Chifukwa cha Chisomo Chake, 1/15

Ntchito ya Mzimu Woyera Pokwaniritsa Cholinga cha Yehova, 4/15

“Olungama Adzawala Ngwee Ngati Dzuwa,” 3/15

Pezani Madalitso Kudzera mwa Mfumu Yotsogoleredwa ndi Mzimu wa Mulungu, 12/15

Pitirizani Kufunafuna Choyamba “Chilungamo Chake,” 10/15

“Pitirizani Kugonjetsa Choipa” mwa Kupewa Kupsa Mtima, 6/15

Sonyezani Kuti Ndinu Wotsatira Weniweni wa Khristu, 1/15

Tidzayenda Mogwirizana ndi Mtima Wathu Wosagawanika, 11/15

Tikukulandirani ku Moyo Wabwino Koposa, 2/15

Ulamuliro wa Satana Utha Posachedwapa, 1/15

Yehova Ndiye Ambuye Wathu Wamkulu, 11/15

Yehova Ndiye Woyeneradi Kulamulira, 1/15

NKHANI ZOSIYANASIYANA

Akhristu Oyambirira Ndiponso Milungu ya Aroma, 5/15

Anauza Mulungu Zakukhosi Kwake (Hana), 7/1

Anthu a M’Baibulo Anakhaladi Nthawi Yaitali Choncho? 12/1

Ayuda ndi Asamariya Ankadana, 10/1

Basamu wa ku Gileadi, 6/1

Chinsinsi Chimene Ungauzeko Ena, 12/1

“Chionetsero cha Kupambana” (2Ak 2:14-16), 8/1

Chipata cha Mudzi, 6/1

Cholembapo Chathabwa (Lu 1:63), 1/1

Golide wa ku Ofiri, 6/1

Kaini Anapeza Kuti Mkazi? 9/1

Kodi Akufa Angathandize Amoyo? 1/1

Kodi Anali Kuikiradi Chikhristu Kumbuyo? 6/1

Kodi Anthu Onse Abwino Amapita Kumwamba? 2/1

Kodi Dziko Lapansi Lidzatha? 1/1

Kodi Dzikoli Latsala Pang’ono Kutha? 8/1

Kodi Mizinda Yothawirako Inali Kobisala Zigawenga? 11/1

Kodi Nyenyezi Zingakuthandizeni? 6/1

Kodi Zinthu Zofunika pa Moyo Zidzatheratu? 3/1

Kukafika Kumalekezero a Dziko Lapansi, 11/1

“Kukula Akukondedwa ndi Yehova” (Samueli), 10/1

Kulankhula Malilime, 10/1

Kulowa Chipembedzo, 11/1

Kuulula Machimo, 9/1

Kuyenda Panyanja Kunali Koopsa M’nthawi ya Paulo, 2/1

Maganizo a Mulungu pa Nkhani ya Mowa, 1/1

Maliko ‘Anali Wofunika Potumikira,’ 3/15

Masunagoge, 4/1

Maulendo Akale Apanyanja Zamchere, 3/1

Milungu Itatu mwa Mulungu Mmodzi, 2/1

“Misanje” Kapena Kuti Malo Okwezeka, 8/1

‘Moyo wa Anthu Uzingokhala Zaka 120’ (Ge 6:3), 12/15

Msewu Umene Paulo Anadutsa (Appia), 1/1

Mumzinda wa Harana Munkachitika Zambiri, 5/15

Mwana Wamwamuna Woyamba Kubadwa, 5/1

Mzimu Woyera, 10/1

N’chifukwa Chiyani Anthu Amachita Zoipa? 9/1

Ndani Amakhala Kumwamba? 12/1

Nyama Yoperekedwa ku Mafano, 10/1

Nyerere Zimakonza Chakudya M’chilimwe, 7/1

Nyumba Zawo (Akhristu Oyambirira), 1/1

“Ogwira Ntchito Zapakhomo” (Tit 2:5), 2/1

Paradaiso Amene Baibulo Limatchula, 12/1

Rabeka, 2/1

Samalani Kuti Musanyengedwe, 9/1

Sanalange Aroni Atapanga Fano, 5/15

Tchimo, 6/1

Timapukusi Tokhala ndi Malemba, 5/1

Ufumu Umene Udzasintha Dziko, 10/1

‘Vinyo Watsopano M’matumba Akale’ (Lu 5:37, 38), 3/1

Woperekera Chikho kwa Mfumu, 7/1

Zakumwa Zoledzeretsa M’nthawi za M’baibulo, 2/1

“Zigawenga” (Mac 21:38), 3/1

Ziphunzitso za Calvin, 9/1

‘Zipsera za Chizindikiro cha Kapolo wa Yesu’ (Aga 6:17), 11/1

YEHOVA

“Adzalola Kuti Um’peze” (1Mb 28:9), 11/1

Alibe Tsankho, 9/1

Amadziwa Mtima, 12/1

Amafuna Kuti Mukhale Otetezeka, 4/15

Amakhululukira a “Mtima Wosweka ndi Wolapa,” 5/1

Amakwaniritsa Malonjezo, 1/1

Amamva Kulira kwa Achisoni, 11/15

Amaona Zabwino mwa Anthu, 7/1

‘Amayang’ana Mumtima,’ 3/1

Anatipatsa Ufulu Wosankha, 9/1

Anawononga Akanani, 1/1

Dzina Lake Linapezeka M’kachisi ku Iguputo, 5/1

Kodi Ali ndi Chiyambi? 7/1

Kodi Amamva Chisoni? 2/1

Kodi Mumamulola Kukufunsani? 4/15

Kodi Mumaona Kuti Ndi Atate Wanu? 2/15

Kodi Watinyanyala? 5/1

Kudziwa Dzina la Mulungu, 7/1

“Mpando Wachifumu Wako Udzakhazikika” (Davide), 4/1

Mwayi Wofanana Wophunzira za Mulungu, 8/1

N’chifukwa Chiyani Analonjeza Moyo Wosatha? 1/1

“Nyamula Mwana Wako” (kamnyamata kaukitsidwa), 8/1

“Wakumva Pemphero,” 10/1

Wokhulupirika, 6/1

YESU KHRISTU

Amene Anakaona Yesu Ali Mwana, 12/1

Amene Analemba za Yesu, 6/1

Anaphunzira Kumvera, 4/1

Anaphunzitsa Zokhudza Angelo, 11/1

Anaphunzitsa Zokhudza Kulambira Koona, 2/1

Anaphunzitsa Zokhudza Kusangalala, 8/1

Chifukwa Chake Anamukana, 12/1

Dziwani Zoona Zake, 4/1

Kodi pa Atumwi, Panali M’bale Wake? 9/1

Kodi Panali Chibale ndi Yohane M’batizi? 9/1

Mayi Wochimwa Akhululukidwa, 8/15

Mikayeli, Mkulu wa Angelo? 4/1

Mmisiri wa Matabwa, 8/1

Munthu Amene Anasintha Dziko, 4/1

N’chifukwa Chiyani Ankatchedwa Khristu? 4/1

Sanapite Mofulumira, 8/1

Sankalowerera Ndale, 7/1

Umboni Wotsimikizira Kuti Yesu Analipodi? 4/1

Zimene Tingachite Kuti Timutsatire, 5/1