Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo

ANA AZAKA ZOSAPITIRIRA ZITATU

Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo

Kodi ndani analenga dziko lapansili?

Kodi ndani analenga nyanja?

Kodi ndani analenga iwe ndi ine?

Kodi ndani analenga gulugufe yemwe ndi wokongola kwambiri?

Yehova Mulungu ndi amene analenga zinthu zonse Chivumbulutso 4:11

ZOTI MAKOLO ACHITE

Phunzitsani mwana wanu zinthu izi:

Kodi dzina la Mulungu ndani?

Kodi Yehova amakhala kuti?

Kodi Yehova analenga zinthu ziti?

Muuzeni mwana wanuyo kuti aloze:

Nyenyezi

Mitambo

Dzuwa

Boti

Dziko

Nyumba

Nyanja

Gulugufe