Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

September 4-10

ESITERE 1-2

September 4-10

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 106

  • Zimene Achinyamata Anzanu Amanena—Maonekedwe: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani nthawi zina zingakhale zovuta kukhala ndi maganizo oyenera pa nkhani ya mmene timaonekera?

    Kodi mfundo ya pa lemba la 1 Petulo 3:​3, 4 ingatithandize bwanji kukhala ndi maganizo oyenera pa nkhani ya mmene timaonekera?

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 56 komanso mawu akumapeto 6 ndi 7

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 101 ndi Pemphero