Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

September 4-10

ESITERE 1-2

September 4-10

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Esitere 2:5—Kodi pali umboni wotani wotsimikizila kuti nkhani ya m’Baibo ya Moredekai ni yoona? (w22.11 31 ¶3-6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Esitere 1:​13-22 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 106

  • Zimene Acicepele Anzanu Amakamba—Maonekedwe Anu: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi, kenako funsani omvela mafunso aya: N’cifukwa ciyani kungakhale kovuta kukhala okhutila na maonekedwe athu?

    Kodi mfundo ya pa 1 Petulo 3:​3, 4 ingatithandize bwanji kudziona moyenela?

  • Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya September.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 56 komanso mfundo zakumapeto 6 na 7

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 101 na Pemphelo