September 4-10

ESITERE 1-2

September 4-10

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Ufumu—Mt 6:​9, 10. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni kabuku kakuti, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 1)

  • Nkhani: (5 min.) w20.11 12-14 ¶3-7—Mutu: Anathandizidwa ndi Yesu Komanso Angelo. (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 106

  • Zimene Achinyamata Anzanu Amanena—Maonekedwe: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani nthawi zina zingakhale zovuta kukhala ndi maganizo oyenera pa nkhani ya mmene timaonekera?

    Kodi mfundo ya pa lemba la 1 Petulo 3:​3, 4 ingatithandize bwanji kukhala ndi maganizo oyenera pa nkhani ya mmene timaonekera?

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 49:1-5

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero