Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere

Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Esitere.]

Esitere anali mtsikana wokongola kwambiri (Est 2:7)

Esitere anakhalabe wodzichepetsa ngakhale pamene anthu ankamutamanda (Est 2:​9, 15; w17.01 25 ¶11; ia 130 ¶15)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zolankhula komanso zochita zanga zimasonyeza kuti ndine munthu wotani?’—w17.01 25 ¶12.