Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere

Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere

[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Esitere.]

Esitere anali mkazi wokongola kwambili (Esitere 2:7)

Esitere anakhalabe wodzicepetsa ngakhale pamene ena anamuyamikila na kumutamanda mopambanitsa (Esitere 2:​9, 15; w17.01 25 ¶11; ia 130 ¶15)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zokamba na zocita zanga zimaonetsa kuti ndine wodzicepetsa?’—w17.01 25 ¶12.