CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere

Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Esitere.]

Esitere anali mtsikana wokongola kwambiri (Est 2:7)

Esitere anakhalabe wodzichepetsa ngakhale pamene anthu ankamutamanda (Est 2:​9, 15; w17.01 4:11; ia 15:15)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zolankhula komanso zochita zanga zimasonyeza kuti ndine munthu wotani?’—w17.01 25 ¶12.