Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Thandizani Ena Kucita Zonse Zimene Angathe Potumikila Yehova

Thandizani Ena Kucita Zonse Zimene Angathe Potumikila Yehova

Moredekai anapeleka citsanzo cabwino pa nkhani yokhala wolimba mtima komanso wokhulupilika kwa Yehova (Esitere 3:​2-4; it-2 431 ¶7)

Iye anathandiza Esitere kuona zimene akanacita pothandiza anthu ake (Esitere 4:​7, 8; it-2 431 ¶9)

Analimbikitsa Esitere kukhala wolimba mtima na kudalila Yehova (Esitere 4:​12-14; ia 133 ¶22-23)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zocita na zokamba zanga zimalimbikitsa ena mumpingo kucita zonse zimene angathe potumikila Yehova?’