Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino

Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino

Esitere anayembekezera nthawi yabwino kuti alankhule (Est 7:2; ia 140 ¶15-16)

Analankhula mwanzeru komanso mwaulemu (Est 7:3; ia 140 ¶17)

Analankhula momveka bwino ndi moona mtima (Est 7:4; ia 141 ¶18-19)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingatsanzire bwanji Esitere ndikamalankhula ndi anthu a m’banja langa?’