Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZELA M’MAWU A MULUNGU

Citsanzo Cimene Tingatengele pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino

Citsanzo Cimene Tingatengele pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino

Esitere anayembekezela nthawi yoyenelela kuti alankhule (Esitere 7:2; ia 140 ¶15-16)

Iye analankhula mosamala komanso mwaulemu (Esitere 7:3; ia 140 ¶17)

Analankhula za kukhosi kwake moona mtima (Esitere 7:4; ia 141 ¶18-19)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ningatengele bwanji citsanzo ca Esitere polankhulana na anthu a m’banja langa?’