Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Samalani ndi Nkhani Zabodza

Samalani ndi Nkhani Zabodza

Zimene Elifazi ankanena zinkaoneka ngati zoona chifukwa anali wamkulu komanso wanzeru (Yob 4:1; it-1 713 ¶11)

Ziwanda zinamutsogolera kuti akapereke uthenga wofooketsa kwa Yobu (Yob 4:​14-16; w05 9/15 26 ¶2)

Zina mwa zomwe Elifazi ananena zinali zoona, koma anazigwiritsa ntchito molakwika (Yob 4:19; w10 2/15 19 ¶5-6)

Dziko la Satanali limafalitsa nkhani zabodza zowononga.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimapeza nthawi yoti nditsimikizire kaye ngati nkhani zimene ndikumva kapena kuwerenga zilidi zoona?’—mrt 32 ¶13-17