Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Samalani na Nkhani Zabodza

Samalani na Nkhani Zabodza

Zimene Elifazi anakamba zinaoneka ngati zoona cifukwa iye anali wamkulu komanso wanzelu (Yobu 4:1; it-1 713 ¶11)

Posonkhezeledwa na ziwanda, Elifazi anakamba mawu olefula kwa Yobu (Yobu 4:​14-16; w05 9/15 26 ¶2)

Zina zimene iye anakamba zinali zoona, koma anazigwilitsa nchito molakwika (Yobu 4:19; w10 2/15 19 ¶5-6)

Dziko la Satanali lapitiliza kufalitsa nkhani zabodza komanso zowononga.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi nimayamba nafufuza kuti nitsimikize ngati nkhani imene namva ni yoona?’—mrt-CN 32 ¶13-17.