Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

October 16-22

YOBU 6-7

October 16-22

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Umoyo Ukafika Poti Simungathenso Kupilila”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 6:29—N’ciyani cingatithandize kupewa kuwaweluza molakwika abale na alongo athu? (w20.04 16 ¶10)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 6:​1-21 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 7)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 11)

  • Nkhani: (Mph. 5) w22.01 12-13 ¶15-18 Mutu: Muziphunzitsa Mogwila Mtima Monga Yakobo—Muziseŵenzetsa Mafanizo Ogwila Mtima. (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU