October 16-22 YOBU 6-7 YAMBANI October 16-22 Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero Mawu Oyamba (1 min.) CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Moyo Ukafika Povuta”: (10 min.) Mfundo Zothandiza: (10 min.) Yob 6:29—N’chiyani chingatithandize kuti tipewe kuweruza molakwika abale athu? (w20.04 16:10) Yankho Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina? Yankho Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 6:1-13 (th phunziro 2) KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 7) Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 11) Nkhani: (5 min.) w22.01 2:15-18—Mutu: Tiziphunzitsa Mogwira Mtima Ngati Yakobo —Tizigwiritsa Ntchito Mafanizo Ogwira Mtima. (th phunziro 8) MOYO WATHU WACHIKHRISTU Nyimbo Na. 144 “Yehova Amapulumutsa Anthu Odzimvera Chisoni”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo. Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 54 Mawu Omaliza (3 min.) Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena October 16-22 UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 16-22, 2023 Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 16-22, 2023 https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023336/univ/art/202023336_univ_sqr_xl.jpg mwb23.9 17