Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Umoyo Ukafika Poti Simungathenso Kupilila

Umoyo Ukafika Poti Simungathenso Kupilila

Pa nthawi ya masautso, Yobu anayelekezela umoyo wake na nchito yokakamiza (Yobu 7:1; w06 3/15 14 ¶10)

Mavuto amene anakumana nawo anam’pangitsa kukamba zonse za mumtima mwake (Yobu 7:11)

Anafika ngakhale pokamba kuti anali kulakalaka kufa (Yobu 7:16; w20.12 16 ¶1)

Ngati inunso muona kuti umoyo wafika poti simungathenso kupilila, mwa pemphelo m’khuthulileni Yehova za mumtima mwanu. Komanso uzankoni mnzanu wokhwima maganizo mmene mumvela. Kucita zimenezi kungakuthandizeni kuyamba kumvako bwino.—g 1/12 16-17.