CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Moyo Ukafika Povuta YAMBANI Moyo Ukafika Povuta Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Pamene ankakumana ndi mayesero, Yobu anayerekezera moyo ndi ntchito yokakamiza (Yob 7:1; w06-CN 3/15 14:10) Mavuto amene Yobu ankakumana nawo anam’chititsa kufotokoza momasuka mmene ankamvera (Yob 7:11) Anafika mpaka ponena kuti akufuna kufa (Yob 7:16; w20.12 51:1) Mukaona kuti moyo wanu wafika povuta kwambiri, muzipemphera kwa Yehova mochokera pansi pamtima, kumuuza zonse zomwe zili mumtima mwanu, komanso muzifotokozera mnzanu wodalirika mmene mukumvera. Imeneyi ikhoza kukhala njira yoyamba imene ingakuthandizeni kuti muyambenso kumva bwino.—g 1/12 16-17. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Moyo Ukafika Povuta UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Moyo Ukafika Povuta Chinenero Chamanja cha ku Malawi Moyo Ukafika Povuta https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023337/univ/art/202023337_univ_sqr_xl.jpg mwb23.9 18