October 23-29
YOBU 8-10
Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 9:32—Kodi tizitani ngati tawerenga nkhani inayake m’Baibulo imene sitikuimvetsa? (w10 10/15 6-7 ¶19-20)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 9:20-35 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 17)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku ka Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo kambiranani naye mwachidule mfundo zimene zili pa mutu wakuti “Zimene Mungachite Kuti Muzipindula ndi Phunziro Lililonse.” (th phunziro 3)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 16 mfundo 6 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzithandiza Anthu Osapembedza Kudziwa Mlengi Wawo”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt “Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira” komanso mutu 1 ¶1-7
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 64 ndi Pemphero