CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana YAMBANI Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Satana amafuna kuti anthu azikhulupirira kuti Yehova ndi amene amachititsa zinthu zoipa (Yob 8:4) Amafunanso kuti tiziganiza kuti Yehova sizimamukhudza ngati tili okhulupirika kapena ayi (Yob 9:20-22; w15-CN 7/1 12:3) Chikondi chokhulupirika cha Yehova chimatithandiza kuti tisamapusitsike ndi mabodza a Satana komanso kuti tikhalabe wokhulupirika (Yob 10:12; Sl 32:7, 10; w21.11 44:14) TAYESANI IZI: Kuti mulimbitse chikhulupiriro chanu, muzifufuza mmene Yehova akukusonyezerani chikondi chokhulupirika, muzilemba zomwe mwapezazo ndipo muziziwerenga mobwerezabwereza. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana Chinenero Chamanja cha ku Malawi Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023340/univ/art/202023340_univ_sqr_xl.jpg mwb23.9 21