Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Njila Zitatu Zopezela Nzelu na Kupindula Nazo

Njila Zitatu Zopezela Nzelu na Kupindula Nazo

Muziyang’ana cilengedwe (Yobu 12:​7-9; w09 4/15 6 ¶17)

Palanani ubwenzi na Akhristu okhulupilika (Yobu 12:12; w21.06 10 ¶10-12)

Phunzilani malamulo a Mulungu na kumawatsatila mu umoyo wanu (Yobu 12:16; it-2 1190 ¶2)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi naphunzila ciyani poceza na Akhristu okhulupilika?’