Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Zimene Tinganene

Zimene Tinganene

ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu n’chiyani?

Lemba: Yes 9:​6, 7 kapena Mt 6:​9, 10

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita chiyani?

MALEMBAWA AKUPEZEKA MU:

ULENDO WOBWEREZA

Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita chiyani?

Lemba: Sl 72:16 kapena Mt 14:​19, 20

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Ufumu wa Mulungu udzayamba liti kulamulira dzikoli?

LEMBA LA SALIMO 72:16 LIKUPEZEKA MU: