Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CITANI KHAMA PA ULALIKI

Makambilano Acitsanzo

Makambilano Acitsanzo

ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu n’ciyani?

Lemba: Yes. 9:​6, 7 kapena Mat. 6:​9, 10

Ulalo: Kodi Ufumu wa Mulungu udzacita ciyani?

PEZANI MALEMBAWA M’THUBOKSI YATHU:

ULENDO WOBWELELAKO

Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu udzacita ciyani?

Lemba: Sal. 72:16 kapena Mat. 14:​19, 20

Ulalo: Ni liti pamene Ufumu wa Mulungu udzalamulila dziko lapansi?

PEZANI SALIMO 72:16 M’THUBOKSI YATHU: