Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2020

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2020

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

BAIBULO

  • Kodi Belisazara anali mfumu ku Babulo? Feb.

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

  • Kodi apolisi apakachisi anali ndani, nanga ntchito yawo inali yotani? Mar.

  • Kodi lemba la Miyambo 24:16 limanena za munthu amene amachita machimo mobwerezabwereza? Dec.

  • Kodi lemba la Mlaliki 5:8 limanena za olamulira a anthu, kapena za Yehova? Sept.

  • Kodi makhalidwe amene “mzimu woyera umatulutsa,” ndi okhawo amene atchulidwa pa Agalatiya 5:22, 23? June

  • Kodi mawu a pa 1 Akorinto 15:29, akutanthauza kuti Akhristu ena kalelo ankabatizidwa m’malo mwa anthu akufa? Dec.

  • Kodi ndi liti pamene Yesu anakhala mkulu wa ansembe, nanga kodi pali kusiyana pakati pa nthawi imene pangano latsopano linakhazikitsidwa komanso nthawi imene linayamba kugwira ntchito? July

MBIRI YA MOYO WANGA

  • “Ife tilipo. Titumizeni” (J. ndi M. Bergame), Mar.

  • Ndadalitsidwa Chifukwa Chotsatira Zimene Ndinaphunzira kwa Anthu Ena (L. Crépeault), Feb.

  • Ndangochita Zimene Ndinayenera Kuchita (D. Ridley), July

  • “Yehova Sanandiiwale” (M. Herman), Nov.

MBONI ZA YEHOVA

  • 1920​—Zimene Zinachitika Zaka 100 Zapitazo, Oct.

  • Anthu Amene Abwerera Kwawo Amapeza Madalitso Ambiri, Nov.

  • Tizichita Zinthu Mogwirizana ndi Kulira Kwa Lipenga, June

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

  • Kudziletsa N’kofunika Kuti Yehova Azisangalala Nafe, June

  • Kufatsa Kodi N’kofunika Bwanji? May

  • Muzichita Khama pa Utumiki Wanu, Dec.

NKHANI ZOPHUNZIRA

  • Atate Wathu Yehova Amatikonda Kwambiri, Feb.

  • “Bwererani Kwa Ine,” June

  • “Dzanja Lako Lisapume,” Sept.

  • “Dzina Lanu Liyeretsedwe,” June

  • Gulu Lankhondo Lochokera Kumpoto, Apr.

  • “Inetu Ndidzafunafuna Nkhosa Zanga,” June

  • “Kodi Akufa Adzaukitsidwa Motani?”Dec.

  • Kodi Ana Anu Akadzakula Azidzatumikira Mulungu? Oct.

  • Kodi Anthu Am’gawo Lanu Mumawaona Bwanji? Apr.

  • Kodi “Mfumu ya Kumpoto” M’nthawi ya Mapeto Ndi Ndani? May

  • Kodi “Mfumu ya Kumpoto” Ndi Ndani Panopa? May

  • Kodi Mukuyembekezera “Mzinda Wokhala ndi Maziko Enieni”? Aug.

  • Kodi Mumadziwa Nthawi Yoyenera Kulankhula? Mar.

  • Kodi Ndinu Ofunitsitsa Kupitiriza Kutsatira Malangizo? Nov.

  • Kodi Ndinu Okonzeka Kubatizidwa? Mar.

  • Kodi Ndinu Okonzeka Kukhala Msodzi wa Anthu? Sept.

  • Kodi Timayamikira Zinthu Zimene Mulungu Anatipatsa? May

  • Kuukitsidwa Kwa Akufa Kumasonyeza Kuti Yehova Ndi Mulungu Wachikondi, Wanzeru Komanso Woleza Mtima, Aug.

  • Limbani Mtima Chifukwa Yehova Akuthandizani, Nov.

  • Maso Ako Aziyang’ana pa Zinthu Zakutsogolo, Nov.

  • Mukhoza Kuthandiza Anthu Komanso Kuwalimbikitsa, Jan.

  • Munthu Amabatizidwa Chifukwa Chokonda Yehova Komanso Kumuyamikira, Mar.

  • Musamadziganizire Kuposa Mmene Muyenera Kudziganizira, July

  • Musamakayikire Kuti Zimene Mumakhulupirira Ndi Zoona, July

  • Muzichita Zinthu Mwanzeru pa Nthawi Yomwe Zinthu Zikuyenda Bwino, Sept.

  • Muzikondana Kwambiri, Mar.

  • Muzilimbikitsa Alongo Mumpingo, Sept.

  • Muzilola Kuti Yehova Azikutonthozani, Feb.

  • Muziona Kuti Anthu Ena Ndi Ofunika Mumpingo, Aug.

  • Muzipewa Nsanje Kuti Muzikhala Mwamtendere, Feb.

  • Muziteteza Zinthu Zimene Mulungu Wakupatsani, Sept.

  • Muzithandiza Ena Kuti Azimvera Malamulo a Khristu, Nov.

  • Muzithandiza Ophunzira Baibulo Anu Kuti Afike Pobatizidwa​—Gawo 1, Oct.

  • Muzithandiza Ophunzira Baibulo Anu Kuti Afike Pobatizidwa​—Gawo 2, Oct.

  • “Mzimu Umachitira Umboni,” Jan.

  • “Ndakutchani Mabwenzi,” Apr.

  • Ndinu Amtengo Wapatali Mumpingo wa Yehova, Aug.

  • “Ndipatseni Mtima Wosagawanika Kuti Ndiope Dzina Lanu,” June

  • “Pamene Ndili Wofooka, M’pamene Ndimakhala Wamphamvu,” July

  • “Pitani Mukaphunzitse Anthu Kuti Akhale Ophunzira Anga,”Jan.

  • Pitirizani Kuyenda m’Choonadi, July

  • Timakhulupirira Kuti Anthu Amene Anamwalira Adzauka, Dec.

  • Timakonda Kwambiri Atate Wathu Yehova, Feb.

  • Tipita Nanu Limodzi, Jan.

  • Tizimvetsera Anthu, Kuwadziwa Komanso Kuwachitira Chifundo, Apr.

  • ‘Tizithamanga Panjirayo Mpaka pa Mapeto,’ Apr.

  • Tiziyamikira Chuma Chosaoneka Chomwe Tili Nacho, May

  • Tiziyenda Modzichepetsa ndi Mulungu, Aug.

  • Yehova Akutsogolera Gulu Lake, Oct.

  • Yehova Amaona Kuti Ndinu Amtengo Wapatali, Jan.

  • Yehova Amapulumutsa Anthu a Mtima Wosweka, Dec.

  • Zimene Tingachite Tikafooka, Dec.

NKHANI ZOSIYANASIYANA

  • Mafumu Awiri Olimbana M’nthawi ya Mapeto, May

  • Umboni wina wosonyeza kuti Aisiraeli anali akapolo ku Iguputo, Mar.

NSANJA YA OLONDA YOGAWIRA

  • Kodi Ufumu Wa Mulungu N’chiyani? Na. 2

  • Kufufuza Choonadi, Na. 1

  • Mulungu Wachikondi Adzatipatsa Madalitso Osatha, Na. 3

GALAMUKANI!

  • Kodi Tsankho Lidzatha? Na. 3

  • Mayankho A Mafunso 5 Okhudza Kuvutika, Na. 2

  • Mungatani Kuti Muchepetse Nkhawa? Na. 1