Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Kalozela wa Nkhani wa Magazini a 2020 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Kalozela wa Nkhani wa Magazini a 2020 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo

NSANJA YA MLONDA YOPHUNZILA

BAIBO

  • Kodi zofukula za m’matongwe zimaonetsa bwanji kuti Belisazara wa ku Babulo anali mfumu? Feb.

UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU

  • Kufatsa—Kodi Khalidweli Limatipindulitsa Bwanji? May

  • Ika Mtima pa Utumiki Wako! Dec.

  • Kudziletsa N’kofunika Kuti Tikondweletse Yehova, June

MBONI ZA YEHOVA

  • 1920—Zaka 100 Zapitazo, Oct.

  • Kulabadila Kulila kwa Lipenga Masiku Ano, June

  • Madalitso Oculuka kwa Amene Amabwelela ku Dziko la Kwawo, Nov.

MBILI YANGA

  • “Ife Tilipo! Titumizeni” (J. na M. Bergame), Mar.

  • Nangocita Zimene N’nayenela Kucita (D. Ridley), July

  • “Yehova Sananiiŵale” (M. Herman), Nov.

  • N’napeza Madalitso Ambili Cifukwa Cophunzila kwa Ofalitsa Acitsanzo Cabwino (L. Crépeault), Feb.

NKHANI ZOSIYANA-SIYANA

  • Umboni woonetsa kuti Aisiraeli anakhalako akapolo ku Iguputo, Mar.

  • Mafumu Aŵili Olimbana M’nthawi Yamapeto, May

MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA

  • Kodi makhalidwe ochulidwa pa Agalatiya 5:22, 23 ndiwo okha “amene mzimu woyela umatulutsa”? June

  • Kodi 1 Akorinto 15:29 Ionetsa kuti Akhristu anali kubatizika cifukwa ca akufa? Dec.

  • Kodi lemba la Mlaliki 5:8 limakamba cabe za olamulila aumunthu kapena limaphatikizaponso Yehova? Sept.

  • Kodi Miyambo 24:16 imakamba za munthu amene amagwela m’chimo mobweleza-bweleza? Dec.

  • Kodi Yesu anakhala liti Mkulu wa Ansembe? Nanga kodi pali kusiyana pakati pa nthawi imene pangano latsopano linayenelezedwa mwalamulo komanso pamene linayamba kugwila nchito? July

  • Kodi apolisi aciyuda a pa kacisi anali ndani? Nanga anali kugwila nchito yanji? Mar.

NKHANI ZOPHUNZILA

  • Citani Zinthu Mwanzelu Panthawi ya Mtendele, Sept.

  • Kuukila kwa Mdani Wocokela Kumpoto! Apr.

  • Kodi Mukuyembekezela “Mzinda Wokhala Ndi Maziko Eni-eni”? Aug.

  • Kodi Ndimwe Wokonzeka Kukhala Msodzi wa Anthu? Sept.

  • Kodi Ndimwe Wokonzeka Kubatizika? Mar.

  • Kodi Mumakhulupililadi Kuti Muli na Coonadi? July

  • “Dzanja Lako Lisapume,” Sept.

  • “Musamadziganizile Kuposa Mmene Muyenela Kudziganizila,” July

  • Kodi Mumayamikila Mphatso Zimene Mulungu Anakupatsani? May

  • Muziwathandiza Alongo Mumpingo, Sept.

  • ‘Pitani Mukaphunzitse Anthu Kuti Akhale Ophunzila Anga,’ Jan.

  • ‘Sungani Bwino Cimene Cinaikidwa M’manja Mwanu,’ Sept.

  • “Kodi Akufa Adzaukitsidwa Motani?” Dec.

  • Kodi Mumawaona Bwanji Anthu a mu Gawo Lanu? Apr.

  • Mmene Tingatsogozele Phunzilo la Baibo Lotsogolela Munthu ku Ubatizo—Gawo 1, Oct.

  • Mmene Tingatsogozele Phunzilo la Baibo Lotsogolela Munthu ku Ubatizo—Gawo 2, Oct.

  • Mmene Tingathandizile Ena Kusunga Malamulo a Khristu, Nov.

  • Mmene Tingagonjetsele Zolefula, Dec.

  • “Nakuchani Mabwenzi,” Apr.

  • “Inetu Ndidzafunafuna Nkhosa Zanga,” June

  • Yehova Akutsogolela Gulu Lake, Oct.

  • Atate Wathu Yehova, Amatikonda Kwambili, Feb.

  • Yehova Amapulumutsa Anthu Olefuka Mtima, Dec.

  • Yehova Mulungu Wathu Amationa Kuti Ndife Ofunika! Jan.

  • Pitilizani Kuyenda m’Coonadi, July

  • Lolani Kuti Yehova Akutonthozeni, Feb.

  • “Dzina Lanu Liyeletsedwe,” June

  • Amvetseleni, Adziŵeni Bwino, Aonetseni Cifundo, Apr.

  • Yang’anani Kutsogolo, Nov.

  • Kukonda Yehova na Kum’yamikila Kudzakusonkhezelani Kubatizika, Mar.

  • Muzikondana Kwambili, Mar.

  • Yesetsani Kulimbikitsa Mtendele mwa Kuthetsa Kaduka, Feb.

  • Lemekezani Wina Aliyense mu Mpingo, Aug.

  • “Bwelelani kwa Ine,” June

  • “Nathamanga Panjilayo Mpaka pa Mapeto,” Apr.

  • Onetsani Kuti Mumayamikila Cuma Cosaoneka, May

  • Limbani Mtima—Yehova Ndiye Mthandizi Wanu, Nov.

  • “Mfumu ya Kumpoto” M’nthawi Yamapeto, May

  • Akufa Adzauka Ndithu—Sitikaika Konse! Dec.

  • Ciukililo Cimaonetsa Kuti Mulungu ni Wacikondi, Wanzelu, Komanso Woleza Mtima, Aug.

  • ‘Mzimu Umacitila Umboni Limodzi Ndi Mzimu Wathu,’ Jan.

  • “Ndipatseni Mtima Wosagawanika Kuti Ndiope Dzina Lanu,” June

  • Muziyenda Modzicepetsa na Mulungu Wanu, Aug.

  • Timam’konda Kwambili Atate Wathu Yehova, Feb.

  • Tipita Nanu Limodzi, Jan.

  • “Pamene Ndili Wofooka, M’pamene Ndimakhala Wamphamvu,” July

  • Kodi Nthawi Yoyenela Kukamba ni Iti? Mar.

  • Kodi “Mfumu ya Kumpoto” Ndani Masiku Ano? May

  • Kodi Ana Anu Adzatumikilabe Yehova Akakula? Oct.

  • Kodi Mudzakhalabe Okonzeka Kusintha? Nov.

  • Mungathe Kulimbikitsa Ena Kwambili, Jan.

  • Na Imwe Muli na Malo mu Mpingo wa Yehova! Aug.

NSANJA YA MLONDA YOGAŴILA

  • Madalitso Osatha Ocokela Kwa Mulungu Wacikondi, No. 3

  • Kufuna-funa Coonadi, No. 1

  • Kodi Ufumu wa Mulungu N’ciani? No. 2

GALAMUKA!

  • Mafunso 5 Pankhani ya Mavuto Ayankhidwa, No. 2

  • Pezani Thandizo Pa Nkhawa Zanu, No. 1

  • Kodi Kuli Mankhwala Othetsela Tsankho? No. 3