Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2021

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2021

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

BAIBULO

  • Kodi zolemba pamwala zimene zapezeka zikugwirizana bwanji ndi Baibulo? Jan.

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

  • Kodi a Mboni ayenera kugwiritsa ntchito ma webusaiti othandiza kupeza wokwatirana naye? July

  • Kodi Paulo ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti: “Mwa chilamulo, ine ndinafa ku chilamulo”? (Agal. 2:19), June

  • N’chifukwa chiyani tiyenera kusamala tikamagwiritsa ntchito mapulogalamu otumizira ndi kulandirira mauthenga? Mar.

  • N’chifukwa chiyani Yesu atatsala pang’ono kufa analankhula mawu a Davide a pa Salimo 22:1? Apr.

  • Tanthauzo la lamulo lakuti “usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako” (Lev. 19:16), Dec.

MBIRI YA MOYO WANGA

  • Ndakhala Ndikusangalala Kutumikira Yehova (J. Kikot), July

  • “Ndaphunzira Zambiri Kuchokera kwa Ena” (L. Breine), May

  • Ndimadalira Yehova Posankha Zochita (D. Yazbek), June

  • Ndinkafuna Moyo Watanthauzo (M. Witholt), Nov.

  • “Panopa Ndimakonda Kwambiri Utumiki” (V. Vicini), Apr.

  • Tinaphunzira Kuti Tisamakane Yehova Akatipatsa Zochita (K. Logan), Jan.

  • Yehova Wakhala ‘Akuwongola Njira Zanga’ (S. Hardy), Feb.

MBONI ZA YEHOVA

  • 1921​—Zomwe Zinachitika Zaka 100 Zapitazo, Oct.

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

  • Kodi Ndinu Wogwira Naye Ntchito Wabwino? Dec.

  • Kukonzanso Ubwenzi Wanu ndi Yehova, Oct.

NKHANI ZOPHUNZIRA

  • Aliyense Mumpingo Angathandize Ophunzira Baibulo Kuti Abatizidwe, Mar.

  • Amene Mwangokwatirana Kumene, Muziika Kutumikira Yehova Pamalo Oyamba, Nov.

  • Buku la Levitiko Limatiphunzitsa Mmene Tingachitire Zinthu ndi Ena, Dec.

  • Chikondi Chimatithandiza Kupirira Ena Akamadana Nafe, Mar.

  • Khamu Lalikulu la Nkhosa Zina Likutamanda Mulungu ndi Khristu, Jan.

  • Kodi Achinyamata Mungatani Kuti Anthu Ena Azikudalirani? Mar.

  • Kodi Chikhulupiriro Chanu Chidzakhala Cholimba? Nov.

  • Kodi Kulapa Kwenikweni N’kutani? Oct.

  • Kodi Mudzakhumudwa N’kusiya Kutsatira Yesu? May

  • Kodi Mudzayembekezera Yehova Moleza Mtima? Aug.

  • Kodi Mungagwire Nawo Ntchito Yothandiza Anthu Kukhala Ophunzira a Yesu? July

  • Kodi Timapindula Bwanji ndi Chikondi Chokhulupirika cha Yehova? Nov.

  • Kodi Tingatani Kuti ‘Tilawe’ Ubwino wa Yehova? Aug.

  • Kodi Yehova Amatiteteza Bwanji? Mar.

  • Malemba Angatithandize Kuti Tizipirira, Mar.

  • “Mukhale Oyera,” Dec.

  • Mungathe Kupulumuka ku Misampha ya Satana, June

  • Munthu Amene Mumamukonda Akasiya Kutumikira Yehova, Sept.

  • Musafooke, Oct.

  • Musakhumudwitse “Tianati,” June

  • Musamakayikire Kuti Munapeza Choonadi, Oct.

  • Musamatekeseke Ndipo Muzidalira Yehova, Jan.

  • “Mutu wa Mkazi Ndi Mwamuna,” Feb.

  • “Mutu wa Mwamuna Aliyense Ndi Khristu,” Feb.

  • Muzikhulupirira Kwambiri Mlengi, Aug.

  • Muzikonda Kwambiri Yehova Komanso Abale ndi Alongo Anu, Sept.

  • Muzimvera Mawu a M’busa Wabwino, Dec.

  • Muziona Kuti Achikulire Okhulupirika Ndi Amtengo Wapatali, Sept.

  • Muziona Kuti Achinyamata Ndi Amtengo Wapatali, Sept.

  • Muzipewa Kuyambitsa Mpikisano Koma Muzilimbikitsa Mtendere, July

  • Muzisangalala ndi Utumiki Wanu, Aug.

  • Muzisangalala ndi Zimene Mukuchita Potumikira Yehova, July

  • Muzithandiza Ophunzira Baibulo Kuti Abatizidwe, June

  • Muzitsanzira Yehova pa Nkhani ya Kupirira, July

  • “Muzitsatira Mapazi Ake Mosamala Kwambiri,” Apr.

  • Muziyamikira Mwayi Wanu Wokhala M’banja la Yehova, Aug.

  • “Ndidzagwedeza Mitundu Yonse ya Anthu,” Sept.

  • Okonda Chilungamo Palibe Chowakhumudwitsa, May

  • Pitirizani ‘Kumumvera,’ Dec.

  • Pitirizani Kuona Utumiki Wanu Moyenera, May

  • Pitirizani Kusonyezana Chikondi Chenicheni, Jan.

  • Pitirizani Kusonyezana Chikondi Chokhulupirika, Nov.

  • Timatumikira Mulungu “Wachifundo Chochuluka,” Oct.

  • Tiziyamikira Mphatso ya Dipo, Apr.

  • Udindo Umene Akulu Ali Nawo Mumpingo, Feb.

  • Yehova Ali Nanu, Simuli Nokha, June

  • Yehova Amakuonani Kuti Ndinu Amtengo Wapatali, Apr.

  • Yehova Amatipatsa Mphamvu, May

  • Zimene Tingachite Kuti Tizisangalalabe Tikakumana ndi Mayesero, Feb.

  • Zimene Tingaphunzire Kwa “Wophunzira Amene Yesu Anali Kumukonda Kwambiri,” Jan.

  • Zimene Tingaphunzire pa Mawu Omaliza a Yesu, Apr.

NKHANI ZOSIYANASIYANA

  • Anthu akale ankagwiritsa ntchito gumbwa popanga maboti, May

  • Misonkho mu nthawi ya Yesu, June

  • Mzinda wa Nineve pambuyo pa nthawi ya Yona, Nov.

  • Zonsezi N’chifukwa cha Kumwetulira Basi Feb.

NSANJA YA OLONDA YOGAWIRA

  • Dziko Labwino Lili Pafupi, Na. 2

  • Kodi Kupemphera N’kothandizadi? Na. 1

  • Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Tsogolo Labwino? Na. 3

GALAMUKANI!

  • Kodi Muyenera Kukhulupirira Kuti Kuli Mlengi?​—Fufuzani, Na. 3

  • Kodi Zipangizo Zamakono Zimakulamulirani? Na. 2

  • Nzeru Zothandiza Kukhala ndi Moyo Wosangalala, Na. 1