Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mlozela Nkhani wa Magazini a 2021 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Mlozela Nkhani wa Magazini a 2021 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo

NSANJA YA MLONDA YOPHUNZILA

BAIBO

  • Kodi zolemba zamakedzana zimacilikiza bwanji zimene Baibo imakamba? Jan.

MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA

  • Kodi Mboni ziyenela kuyaona bwanji mawebusaiti opezelapo zibwenzi? July

  • Kodi mtumwi Paulo anatanthauza ciani pamene anakamba kuti: “Mwa cilamulo, ine ndinafa ku cilamulo”? (Agal. 2:19), June

N’cifukwa ciani tiyenela kusamala poseŵenzetsa njila zotumizilana mauthenga? Mar.

  • N’cifukwa ciani Yesu atangotsala pang’ono kufa anagwila mawu Salimo 22:1? Apr.

Zimene lamulo lakuti “usacite kanthu kalikonse kuti uphetse” mnzako litanthauza (Lev. 19:16), Dec.

  • MBILI YANGA

  • “Naphunzila Zambili kwa Ena!” (L. Breine), May

  • “Tsopano Nimaukonda Ulaliki!” (V. Vicini), Apr.

  • N’nali Kufuna-funa Umoyo Waphindu (M. Witholt), Nov.

  • Napeza Cimwemwe Potumikila Yehova (J. Kikot), July

  • Pa Zonse Zimene Nimasankha, Nimaika Yehova Patsogolo (D. Yazbek), June

  • Tinaphunzila Kusakana Utumiki Umene Yehova Watipatsa (K. Logan), Jan.

Yehova ‘Wawongola Njila Zanga’ (S. Hardy), Feb.

  • MBONI ZA YEHOVA

  • 1921—Zaka 100 Zapitazo, Oct.

  • NKHANI ZOPHUNZILA

  • Abale Acinyamata—Kodi Mungacite Ciani Kuti Ena Azikudalilani? Mar.

Cikondi Cimatithandiza Kupilila Cidani, Mar.

  • Gwilani Coonadi Mwamphamvu Komanso Motsimikiza, Oct.

  • Inu Okwatilana Caposacedwa—Ikani Mtima Wanu pa Kutumikila Yehova, Nov.

  • Khalani Osatekeseka Ndipo Dalilani Yehova, Jan.

  • Khamu Lalikulu la Nkhosa Zina Litamanda Mulungu na Khristu, Jan.

  • Kodi Cikhulupililo Canu Cidzakhala Colimba Motani? Nov.

Kodi Cikondi Cosasintha ca Yehova N’ciani? Nov.

  • Kodi Kulapa Kwenikweni N’ciani? Oct.

  • Kodi Mudzapunthwa Cifukwa ca Yesu? May

  • Kodi Mudzayembekezela Yehova Moleza Mtima? Aug.

  • Kodi Mungathandize pa Nchito Yopanga Ophunzila? July

  • Kondwelani na Mmene Mukupitila Patsogolo! July

  • Kumvetsa Tanthauzo la Umutu Mumpingo, Feb.

  • ‘Laŵani’ Ubwino wa Yehova—Motani? Aug.

  • Limbitsani Cikhulupililo Canu mwa Mlengi, Aug.

  • Mmene Tingakhalilebe Acimwemwe Popilila Mayeso, Feb.

  • Mmene Tingapezele Mphamvu m’Malemba, Mar.

  • Monga Mpingo, Thandizani Maphunzilo a Baibo Kupita Patsogolo Kuti Akabatizike, Mar.

  • Mungathe Kuwonjoka m’Misampha ya Satana! June

  • Munthu Amene Timakonda Akasiya Yehova, Sept.

  • Musaleke Kulimbikila! Oct.

  • Musapunthwitse “Tianati,” June

  • “Mutu wa Mkazi Ndi Mwamuna,” Feb.

  • “Mutu wa Mwamuna Aliyense Ndi Khristu,” Feb.

  • “Muzikhala Oyela,” Dec.

  • Muzikondwela na Mwayi Wanu wa Utumiki, Aug.

  • Muziona Okalamba Okhulupilika Kuti Ni Ofunika, Sept.

  • Muziyamikila Malo Anu M’banja la Yehova, Aug.

  • Muziyamikila Mphamvu za Acinyamata, Sept.

  • Mvelani Mawu a M’busa Wabwino, Dec.

  • “Ndigwedeza Mitundu Yonse ya Anthu,” Sept.

  • Olungama Palibe Cowakhumudwitsa, May

  • Pewani Kuyambitsa Mzimu Wampikisano—Limbikitsani Mtendele, July

  • Pitilizani ‘Kumumvela,’ Dec.

  • Pitilizani Kukhala na Maganizo Oyenela pa Ulaliki Wanu, May

  • Pitilizani Kuonetsana Cikondi Ceni-ceni, Jan.

  • Pitilizani Kuonetsana Cikondi Cosasintha, Nov.

  • Pitilizani Kuyamikila Dipo, Apr.

  • Tengelani Citsanzo ca Yehova pa Kupilila, July

  • Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo Kuti Akakhale Ophunzila Obatizika, June

  • Timatumikila Mulungu “Wacifundo Coculuka,” Oct.

  • ‘Tsatilani Mapazi Ake Mosamala Kwambili,’ Apr.

  • Yandikilani Banja Lanu Lauzimu, Sept.

  • Yehova Adzakupatsani Mphamvu, May

  • Yehova Adzakutetezani—Motani? Mar.

  • Yehova Ali Namwe, Simuli Mwekha, June

  • Yehova Amakukondani Kwambili! Apr.

  • Zimene Timaphunzila m’Buku la Levitiko pa Nkhani Yocita Zinthu na Ŵena, Dec.

  • Zimene Tingaphunzile Kwa “Wophunzila Amene Yesu Anali Kumukonda Kwambili,” Jan.

  • Zimene Tingaphunzile pa Mawu Othela a Yesu, Apr.

  • NKHANI ZOSIYANA-SIYANA

  • Gumbwa anali kugwilitsidwa nchito kupanga ngalawa m’nthawi za m’Baibo, May

  • Misonkho m’nthawi ya Yesu, June

  • Nineve Yona atamwalila, Nov.

  • Zonsezi Zinatheka Cifukwa ca Kumwetulila! Feb.

  • UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU

  • Kodi Ndinu Wanchito Mnzake Wabwino? Dec.

  • Konzaninso Ubwenzi Wanu na Yehova, Oct.

NSANJA YA MLONDA YOGAŴILA

  • Dziko Labwino Lili Pafupi, Na. 2

  • Mungacite Ciani Kuti Mukhale na Tsogolo Labwino? Na. 3

  • N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupemphela? Na. 1

GALAMUKA!

  • Kodi Muyenela Kukhulupilila kuti Kuli Mlengi? Na. 3

  • Kodi Ndinu Kapolo wa Zipangizo Zamakono? Na. 2

  • Nzelu Zokuthandizani Kukhala na Umoyo Wacimwemwe, Na. 1