Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Yehova Amakhululuka

Yehova Amakhululuka

Tonsefe timalakwitsa zinthu koma Yehova amakhala wokonzeka kutikhululukira nthawi zonse. Tiyeni tione mmene amachitira zimenezi.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Yehova Amakhululuka

Tikalakwitsa chinachake, kodi tizinyanyala? Tiyeni tione zimene Kalebe waphunzira m’nkhani inayake ya m’Baibulo.

ZOCHITA PA GAWO LA KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Posita: Yehova Amakhululuka

Pangani dawunilodi ndi kusindikiza posita imene ikutiuza mmene Yehova amakhululukira anthu okhulupirika akalakwitsa zinazake.

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.