Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.
Canada
13893 Highway 7
GEORGETOWN ON L7G 4S4
CANADA
+1 905-873-4100
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 10:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 15:00hrs.
Nthawi yoona malo: Maola aŵili
Zimene Timacita
Timasindikiza magazini oposa 255 miliyoni caka ciliconse. Ndiponso timatumiza matani oposa 6,000 a mabuku ndi magazini a zinenelo pafupifupi 300.