Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Zimbabwe

Plot 14 of Good Hope

Beema Road

Mount Hampden

HARARE

ZIMBABWE

+263 4-2910591

+263 712-604892

+263 772-472403

+263 772-472404

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timacita

Ofesi ya ku Zimbabwe imayang’anila nchito ya Mboni za Yehova zoposa 39,000 m’dzikolo. Pa ofesiyi amamasulilanso mabuku ofotokoza Baibulo m’zinenelo zambili kuphatikizapo Cishona, Cindebele, ndi cinenelo ca manja ca ku Zimbabwe.

Tengani kapepala koonetsa malo.