Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Zimene Mungachite Kuti Muzipewa Mayesero

Mungaphunzire zambiri pa nkhani ya Yosefe ndi mkazi wa Potifara. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.