Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Yakobo

Koperani khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti muphunzire zambiri za Yakobo, yemwe anali mwana wa Isaki ndi Rabeka. Sindikizani, dulani, pindani pakati ndi kusunga.