Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Mmene Zochita za Angelo Komanso Ziwanda Zimakhudzira Moyo Wathu (Gawo 2)

N’chifukwa chiyani Yehova amaletsa anthu kuti azichita chilichonse chokhudza kukhulupirira mizimu? Kodi tingadziteteze bwanji kwa ziwanda zimene zimafuna kutisocheretsa?