Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kodi Ungatani Kuti Ukhale Woleza Mtima?

Kodi Ungatani Kuti Ukhale Woleza Mtima?

Ukhoza kukhala woleza mtima ngati Yehova. Tiyeni tione mmene ungachitire zimenezi.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Ukhoza Kukhala Woleza Mtima

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene zinamuthandiza Kalebe kuti akhale woleza mtima.

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.