Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Kulambira Kumene Mulungu Amavomereza (Gawo 2)

Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’mutu 15 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Kodi kungokhulupirira kuti kuli Mulungu n’kokwanira? Kapena kodi pali zinthu zinanso zimene amafuna kuti atumiki ake azichita?