Onani zimene zilipo

KHALANI MASO!

Kodi Masamba a Mcezo Akuwononga Mwana Wanu?

Mmene Baibo Ingathandizile Makolo.

 

Dziwani Zambili

Ŵelengani Baibo pa Intaneti

Onani mbali zosiyanasiyana za Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano, Baibo imene ni yolondola komanso yosavuta kuŵelenga.

Ŵelengani Baibo pa Intaneti

Onani mbali zosiyanasiyana za Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano, Baibo imene ni yolondola komanso yosavuta kuŵelenga.

Zoikidwamo posacedwa: mavidiyo, nyimbo, nkhani, komanso nyuzi.

Onani Zatsopano

Yambani Kuphunzila Baibo

Landilani maphunzilo a Baibo okambilana na munthu wina kwaulele.

Pemphani kuti wa Mboni adzakucezeleni

Kambilanani nkhani ya m’Baibo na Mboni za Yehova, kapena laŵani maphunzilo a Baibo amene timapeleka.

Kapezekemponi pa Misonkhano ya Mboni za Yehova

Fufuzani kumene timakumana komanso mmene timalambilila. Onse ni olandilidwa ndipo sipakhala kuyendetsa mbale ya zopeleka.

Mboni za Yehova—Kodi Ndife Anthu Otani?

Ngakhale kuti timacokela kosiyana-siyana ndipo timakamba zinenelo zosiyana-siyana, timagwilizana cifukwa tili na colinga cimodzi. Cimene timafuna kwambili ni kulemekeza Yehova, Mwiniwake Baibo na Mlengi wa zinthu zonse. Timalimbikila kutsatila Yesu Kristu ndipo timanyadila kukhala Akristu. Aliyense wa ife amapatula nthawi yothandiza anthu kudziŵa Baibo na Ufumu wa Mulungu. Cifukwa cakuti timalalikila za Yehova Mulungu na Ufumu wake, timachedwa Mboni za Yehova.

Onani zili pa webusaiti yathu. Ŵelengani Baibo pa intaneti. Tidziŵeni bwino ife na zimene timakhulupilila.

 

A Mboni za Yehova aŵili alalikila munthu m’munda wa mpunga.