Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Phunziro 29: Uzidzichepetsa

Phunziro 29: Uzidzichepetsa

Yehova amakonda anthu odzichepetsa. Kodi ungatani kuti uzidzichepetsa?

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZOCHITA PA GAWO LA KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Uzidzichepetsa

Phunzirani zokhudza kudzichepetsa kuchokera kwa anthu osiyanasiyana otchulidwa m’Baibulo.

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.