M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akupereka lipoti la mmene zinthu zikuyendera pa nthawi ya mliriyi komanso akutilimbikitsa kuti tipitirizebe kukhala maso mwauzimu..
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo zomwe zingatithandize kulimbana ndi nkhawa zomwe tingakhale nazo chifukwa cha nkhondo yomwe ikuchitika m’mayiko akum’mawa kwa Europe.