NSANJA YA OLONDA April 2010 Munthu Amene Anasintha Dziko Uthenga wa Yesu Khristu Ndi Wamphamvu Kwambiri Kodi Yesu Anati Iye Ndi Ndani? Kodi Yesu Anaphunzitsa Chiyani za Mulungu? Kodi Yesu Anaphunzitsa Chiyani za Ufumu wa Mulungu? Kodi Uthenga wa Yesu Khristu Umakukhudzani Bwanji? Dziwani Zoona Zake za Yesu Kodi Mukudziwa? Sunagoge Anali Malo Amene Yesu ndi Ophunzira Ake Ankakonda Kulalikira Kodi Yesu Amatchedwanso Mikayeli, Mkulu wa Angelo? “Mpando Wachifumu Wako Udzakhazikika” Mbuye Wake Anam’phunzitsa Kukhululukira Ena Kodi Baibulo Limafotokoza Zonse Zokhudza Yesu? PHUNZITSANI ANA ANU Yesu Anaphunzira Kumvera