NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA December 2014

M’magazini ino muli nkhani zophunzila za mlungu wa February 2 mpaka wa March 1, 2015.

Njilayo ‘Anali Kuidziŵa’

M’bale Guy H. Pierce, amene anali membala wa Bungwe Lolamulila la Mboni za Yehova anamwalila pa Ciŵili, March 18, 2014.

Yehova Amadalitsa Kwambili Anthu Ofunitsitsa Kupeleka

Tingatengepo phunzilo lofunika kwambili pa lamulo limene Mulungu anapatsa Aisilaeli lokhuza zopeleka.

‘Mvelani ndi Kumvetsa Tanthauzo Lake’

Yesu anafotokoza fanizo la kanjele ka mpilu, la zofufumitsa, la wamalonda woyendayenda, ndi la cuma cobisika. Kodi mafanizo amenewa amatanthauza ciani?

Kodi ‘Mumamvetsa Tanthauzo la Malemba’?

Kodi fanizo la Yesu la wofesa mbeu amene amagona, la khoka, ndi la mwana wolowelela limatanthauza ciani?

Kodi mukukumbukila?

Mafunso 12 amene ali m’nkhani ino akuthandizani kuona ngati mukukumbukila zimene tinaphunzila m’magazini a Nsanja ya Mlonda kuyambila ya June mpaka ya December 2014.

Kodi Muyenela Kusintha Maganizo Anu?

Zosankha zina simufunika kuzisintha koma zina mungazisinthe. Mungadziŵe bwanji kuti mufunika kusintha kapena ai?

Mafunso Ocokela Kwa Aŵelengi

Kodi Yeremiya anali kutanthauza ciani pamene ananena kuti Rakele anali kulilila ana ake?

Tikhale Ogwilizana Pamene Mapeto a Dzikoli Ayandikila

Zitsanzo zinai za m’Baibulo zimaonetsa kufunika kwa mgwilizano, ndiponso cifukwa cake mgwilizano udzakhala wofunika kwambili mtsogolo.

Mlozela Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Mlonda a 2014

Mndandanda wa nkhani zofalitsidwa mu magazini Ophunzila ndi Ogaŵila a 2014.