NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) November 2015

Magaziniyi ili ndi nkhani zophunzira kuyambira December 28, 2015, mpaka January 31, 2016.

Muziphunzitsa Ana Anu Aang’ono Kuti Azitumikira Yehova

Makhalidwe atatu amene Yesu ankasonyeza pophunzitsa, angakuthandizeni kuti muziphunzitsa bwino ana anu.

Muziphunzitsa Ana Anu Achinyamata Kuti Azitumikira Yehova

Kodi mungathandize bwanji mwana wanu kuti ayambe kukonda zinthu zauzimu adakali wachinyamata?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi pali umboni wotani wosonyeza kuti mzinda wakale wa Yeriko unagonjetsedwa m’kanthawi kochepa?

Tiziyamikira Zimene Yehova Amatipatsa

Baibulo limasonyeza kuti munthu angapereke nthawi, mphamvu komanso zinthu zake pa zifukwa zoyenera kapena zosayenera.

Yehova Ndi Mulungu Wachikondi

Kodi Yehova wasonyeza bwanji kuti amakonda anthu?

Kodi ‘Mumakonda Anzanu Ngati Mmene Mumadzikondera Nokha’?

Mungatsatire lamulo la Yesu limeneli m’banja mwanu, mu mpingo wanu komanso mukamalalikira.

Zimene Zachitika M’zaka 100 Zimene Ufumu Wakhala Ukulamulira

Kodi taphunzitsidwa njira zitatu ziti zotithandiza kuti tizilalikira bwino za Ufumu wa Mulungu?

KALE LATHU

“Musalole Kuti Chilichonse Chikulepheretseni”

Atumiki a nthawi zonse a ku France a zaka za m’ma 1930 anali zitsanzo pa nkhani ya kudzipereka komanso kupirira.